Dec 10 2024

Kuthetsa nkhanza ndi udindo wa aliyense

Ngati njira imodzi yochepetsera nkhanza zomwe ana achichepere akukumana nazo m’madela omwe timakhala bungwe la Starlight, mogwirizana ndi Police ya mzinda wa Blantyre ikumema anthu okhala m’madela amu mzindawu kuti adzineneza ku Police anthu omwe akuchitira nkhanza ana omwe amakhala nawo.

FB_IMG_1726212829581

Our Maps

© 2026 Copyright by Starlightmw